A Christian’s Heart

Adrian Asahel Chitawo

Intro
(Inkosi)
(with the Dada)
Get your bibles ready, I’m about to preach
Asah

Verse 1
Atate mumamvera mesa?
Mesa kuchimwa osaziwano sikuku yesani?
Mesa mwana Amakula pokhapokha akamamudyesa
Koma akhristu anu kulowa mkachisi akumatilesa
Ati ndife osochela
Ndipo tinazolowera zachikunja
Nde kusintha kwathu akuti nkosatheka
Are they perfect or maybe anangobadwa oyelesesa???
Ndipo Nkhondo ya chipembezo ikusowa oyilesesa
Kodi mesa!
You're the judge and you provide the grace huh?
They telling me I'm on thе path to hell because of my hairstylе
Ndikamagwa akumandi jeda, ndikazuka ati ndine onyenga
They said I'm less of a Christian because of all these mistakes now
Sindikumvesa
(Mvesa)
Mtima wa mkhristu
Ndosiyana kwambili ndi mtima wa Yesu Khristu
They be happy to see you fall but they choose to rebuke you
Ain't nobody clean as a whistle, I don't try to please the people
And miracles are what is driving all of your people
A church is post to be a hospital for all these cripples
But now it is a money-making building
Can you speak Lord
A church boy is dirtier these days than a street boy
I'm not speaking out of rage
These days, Christianity is just a cage
There's more religion, than preaching
They prolly switching the scriptures
And hating every sinner
So, I stay away from church

Curiosités sur la chanson A Christian’s Heart de Asvhel

Quand la chanson “A Christian’s Heart” a-t-elle été lancée par Asvhel?
La chanson A Christian’s Heart a été lancée en 2022, sur l’album “Church Boi Ep”.
Qui a composé la chanson “A Christian’s Heart” de Asvhel?
La chanson “A Christian’s Heart” de Asvhel a été composée par Adrian Asahel Chitawo.

Chansons les plus populaires [artist_preposition] Asvhel

Autres artistes de